2 Samueli 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Sauli ndi Yonatani,+ anthu okondeka ndi osangalatsa pamene anali ndi moyo,Ngakhale pa imfa yawo sanasiyane.+Iwo anali aliwiro kuposa chiwombankhanga,+Amphamvu kuposa mikango.+ 1 Mafumu 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero, mneneri wokalambayo anakaika mtembowo m’manda ake. Ndipo anapitiriza kumulira+ kuti: “Kalanga ine, m’bale wanga!”
23 Sauli ndi Yonatani,+ anthu okondeka ndi osangalatsa pamene anali ndi moyo,Ngakhale pa imfa yawo sanasiyane.+Iwo anali aliwiro kuposa chiwombankhanga,+Amphamvu kuposa mikango.+
30 Atatero, mneneri wokalambayo anakaika mtembowo m’manda ake. Ndipo anapitiriza kumulira+ kuti: “Kalanga ine, m’bale wanga!”