Yeremiya 48:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Ponena za Mowabu+ Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti:+ “Tsoka Nebo+ chifukwa wafunkhidwa! Mzinda wa Kiriyataimu+ walandidwa ndipo anthu ake achita manyazi. Anthu okhala m’malo okwezeka achitetezo achita manyazi ndipo achita mantha.+ Ezekieli 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza kuti Mowabu+ ndi Seiri+ anena kuti: “Taonani! Nyumba ya Yuda ili ngati mitundu ina yonse ya anthu,”+
48 Ponena za Mowabu+ Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti:+ “Tsoka Nebo+ chifukwa wafunkhidwa! Mzinda wa Kiriyataimu+ walandidwa ndipo anthu ake achita manyazi. Anthu okhala m’malo okwezeka achitetezo achita manyazi ndipo achita mantha.+
8 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza kuti Mowabu+ ndi Seiri+ anena kuti: “Taonani! Nyumba ya Yuda ili ngati mitundu ina yonse ya anthu,”+