Salimo 79:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atsanula magazi awo ngati madziKuzungulira Yerusalemu yense, ndipo palibe wowaika m’manda.+ Yesaya 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma iweyo watayidwa popanda kuikidwa m’manda,+ ngati mphukira yonyansa imene ili pakati pa anthu akufa ophedwa ndi lupanga, amene akutsikira kumiyala ya m’dzenje.+ Watayidwa ngati mtembo wopondedwapondedwa.+
19 Koma iweyo watayidwa popanda kuikidwa m’manda,+ ngati mphukira yonyansa imene ili pakati pa anthu akufa ophedwa ndi lupanga, amene akutsikira kumiyala ya m’dzenje.+ Watayidwa ngati mtembo wopondedwapondedwa.+