Yeremiya 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Yeremiya anabwerako ku Tofeti+ kumene Yehova anamutuma kuti akalosere. Kenako anakaima m’bwalo la nyumba ya Yehova ndi kuuza anthu onse kuti:+ Yohane 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yesu anamuyankha kuti: “Ndalankhula poyera ku dzikoli. Nthawi zonse ndinali kuphunzitsa m’masunagoge ndi m’kachisi,+ kumene Ayuda onse anali kusonkhana, ndipo sindinalankhule kanthu mseri. Machitidwe 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Pitani, ndipo mukaimirire m’kachisi ndi kupitiriza kuuza anthu zoyenera kuchita kuti adzapeze moyo umene ukubwerawo.”+
14 Ndiyeno Yeremiya anabwerako ku Tofeti+ kumene Yehova anamutuma kuti akalosere. Kenako anakaima m’bwalo la nyumba ya Yehova ndi kuuza anthu onse kuti:+
20 Yesu anamuyankha kuti: “Ndalankhula poyera ku dzikoli. Nthawi zonse ndinali kuphunzitsa m’masunagoge ndi m’kachisi,+ kumene Ayuda onse anali kusonkhana, ndipo sindinalankhule kanthu mseri.
20 “Pitani, ndipo mukaimirire m’kachisi ndi kupitiriza kuuza anthu zoyenera kuchita kuti adzapeze moyo umene ukubwerawo.”+