Deuteronomo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti ndi mtundu winanso uti wamphamvu+ umene milungu yake ili pafupi nawo, monga mmene Yehova Mulungu wathu alili pafupi ndi ife, tikamaitanira pa iye+ nthawi zonse? Yesaya 55:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu funafunani Yehova pamene iye akupezekabe.+ Muitaneni akadali pafupi.+
7 Pakuti ndi mtundu winanso uti wamphamvu+ umene milungu yake ili pafupi nawo, monga mmene Yehova Mulungu wathu alili pafupi ndi ife, tikamaitanira pa iye+ nthawi zonse?