Yeremiya 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ukanene kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova, inu mfumu ya Yuda amene mwakhala pampando wachifumu wa Davide.+ Mumve mawu amenewa inuyo, atumiki anu komanso anthu anu amene amalowa pazipata izi.+ Yeremiya 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno m’chaka chimenecho, chaka chachinayi, m’mwezi wachisanu, kuchiyambi kwa ufumu wa Zedekiya+ mfumu ya Yuda, Hananiya+ mwana wa Azuri, mneneri wa ku Gibeoni,+ anauza Yeremiya m’nyumba ya Yehova pamaso pa ansembe ndi anthu onse kuti:
2 Ukanene kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova, inu mfumu ya Yuda amene mwakhala pampando wachifumu wa Davide.+ Mumve mawu amenewa inuyo, atumiki anu komanso anthu anu amene amalowa pazipata izi.+
28 Ndiyeno m’chaka chimenecho, chaka chachinayi, m’mwezi wachisanu, kuchiyambi kwa ufumu wa Zedekiya+ mfumu ya Yuda, Hananiya+ mwana wa Azuri, mneneri wa ku Gibeoni,+ anauza Yeremiya m’nyumba ya Yehova pamaso pa ansembe ndi anthu onse kuti: