Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 43:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndidzauza kumpoto kuti,+ ‘Abwezere kwawo!’ ndipo ndidzauza kum’mwera kuti, ‘Usawakanize! Bweretsa ana anga aamuna kuchokera kutali, ndi ana anga aakazi kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+

  • Yeremiya 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pita, ndipo ukalengeze mawu awa kumpoto+ kuti:

      “‘Yehova wanena kuti: “Bwerera Isiraeli wopanduka iwe. Sindidzakuyang’anani mokwiya anthu inu+ pakuti ndine wokhulupirika,”+ watero Yehova.+ “Sindidzakhala wokwiya mpaka kalekale.+

  • Yeremiya 23:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma adzalumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa a m’nyumba ya Isiraeli ndi kuwabweretsa kuno kuchokera m’dziko la kumpoto komanso kuchokera m’mayiko onse kumene ndinawabalalitsira’ ndipo adzakhala m’dziko lawo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena