Levitiko 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Usalole kuti aliyense mwa ana ako aperekedwe+ kwa Moleki.*+ Usanyoze+ dzina la Mulungu wako mwa njira imeneyi. Ine ndine Yehova.+ Levitiko 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma nzikazo zikanyalanyaza mwadala munthu ameneyo mwa kusamupha+ pamene wapereka aliyense mwa ana ake kwa Moleki,
21 “‘Usalole kuti aliyense mwa ana ako aperekedwe+ kwa Moleki.*+ Usanyoze+ dzina la Mulungu wako mwa njira imeneyi. Ine ndine Yehova.+
4 Koma nzikazo zikanyalanyaza mwadala munthu ameneyo mwa kusamupha+ pamene wapereka aliyense mwa ana ake kwa Moleki,