8 Ndipo ndinawauza kuti: “Ife tachita zonse zimene tikanatha mwa kuwombola+ abale athu achiyuda amene anagulitsidwa kwa anthu a mitundu ina. Kodi pa nthawi imodzimodziyo inu mukugulitsa abale anu,+ ndipo kodi ife tiwawombole?” Pamenepo anangokhala chete, kusowa chonena.+