Levitiko 25:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “‘M’bale wanu akasauka pakati panu+ ndipo sangathe kudzisamala, muzim’thandiza.+ Iye ayenera kukhala ndi moyo mmene mlendo wokhala pakati panu+ alili ndi moyo. Deuteronomo 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Wina mwa abale ako akasauka pakati panu, mu umodzi mwa mizinda yanu, m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, usamuumire mtima kapena kumuumitsira dzanja lako.+ Yeremiya 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kuti aliyense wa iwo amasule wantchito wake wamwamuna kapena wamkazi, mwamuna wachiheberi+ kapena mkazi wachiheberi ndi kumulola kupita kwawo mwaufulu. Anachita izi kuti anthuwo asagwiritsenso ntchito Myuda mnzawo, amene ndi m’bale wawo ngati wantchito wawo.+
35 “‘M’bale wanu akasauka pakati panu+ ndipo sangathe kudzisamala, muzim’thandiza.+ Iye ayenera kukhala ndi moyo mmene mlendo wokhala pakati panu+ alili ndi moyo.
7 “Wina mwa abale ako akasauka pakati panu, mu umodzi mwa mizinda yanu, m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, usamuumire mtima kapena kumuumitsira dzanja lako.+
9 kuti aliyense wa iwo amasule wantchito wake wamwamuna kapena wamkazi, mwamuna wachiheberi+ kapena mkazi wachiheberi ndi kumulola kupita kwawo mwaufulu. Anachita izi kuti anthuwo asagwiritsenso ntchito Myuda mnzawo, amene ndi m’bale wawo ngati wantchito wawo.+