Yeremiya 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi iliyonse imene ndinganene kuti ndizula, kugwetsa ndi kuwononga mtundu uliwonse wa anthu kapena ufumu,+ Ezekieli 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Iwe mwana wa munthu, lirira khamu la ku Iguputo ndi kulengeza kuti lidzatsikira kumanda.+ Dzikolo ndi anthu a mitundu yamphamvu adzatsikira pansi pa nthaka+ limodzi ndi amene akutsikira kudzenje.+
7 Pa nthawi iliyonse imene ndinganene kuti ndizula, kugwetsa ndi kuwononga mtundu uliwonse wa anthu kapena ufumu,+
18 “Iwe mwana wa munthu, lirira khamu la ku Iguputo ndi kulengeza kuti lidzatsikira kumanda.+ Dzikolo ndi anthu a mitundu yamphamvu adzatsikira pansi pa nthaka+ limodzi ndi amene akutsikira kudzenje.+