Yeremiya 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 kuchokera tsiku limene makolo anu anatuluka m’dziko la Iguputo kufikira lero.+ Ndinapitiriza kukutumizirani atumiki anga onse aneneri, tsiku ndi tsiku ndinali kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza.+ Yeremiya 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova anakutumizirani atumiki ake onse aneneri. Anali kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza, koma inu simunawamvere+ kapena kutchera khutu lanu kuti mumvetsere.+
25 kuchokera tsiku limene makolo anu anatuluka m’dziko la Iguputo kufikira lero.+ Ndinapitiriza kukutumizirani atumiki anga onse aneneri, tsiku ndi tsiku ndinali kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza.+
4 Yehova anakutumizirani atumiki ake onse aneneri. Anali kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza, koma inu simunawamvere+ kapena kutchera khutu lanu kuti mumvetsere.+