Yeremiya 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nenani zimenezi anthu inu. Nenani zimenezi kwa anthu a mitundu ina. Lengezani zimene zidzagwera Yerusalemu.” “Alonda akubwera kuchokera kudziko lakutali+ ndipo adzalengeza uthenga wa zimene zidzagwera mizinda ya Yuda. Yeremiya 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “‘Ana a Isiraeli ndi ana a Yuda akhala akuchita zoipa pamaso panga kuyambira pa ubwana wawo.+ Ana a Isiraeli akundikhumudwitsa ndi ntchito za manja awo,’+ watero Yehova.
16 Nenani zimenezi anthu inu. Nenani zimenezi kwa anthu a mitundu ina. Lengezani zimene zidzagwera Yerusalemu.” “Alonda akubwera kuchokera kudziko lakutali+ ndipo adzalengeza uthenga wa zimene zidzagwera mizinda ya Yuda.
30 “‘Ana a Isiraeli ndi ana a Yuda akhala akuchita zoipa pamaso panga kuyambira pa ubwana wawo.+ Ana a Isiraeli akundikhumudwitsa ndi ntchito za manja awo,’+ watero Yehova.