2 Mafumu 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Hilikiya+ mkulu wa ansembe anauza Safani+ mlembi+ kuti: “Ndapeza buku la chilamulo+ m’nyumba ya Yehova!” Choncho Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani, ndipo iye anayamba kuliwerenga. Yeremiya 39:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo anatuma anthuwo kuti akatenge Yeremiya m’Bwalo la Alonda+ ndi kumupereka kwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ kuti apite naye kunyumba kwake, kuti Yeremiyayo akakhale pakati pa anthu akwawo. Ezekieli 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndinaonanso akuluakulu 70+ a nyumba ya Isiraeli ataimirira. Yaazaniya mwana wa Safani+ anali ataima pakati pawo. Iwo anaima pamaso pa zojambulazo, aliyense atanyamula chiwaya chofukizira nsembe m’manja mwake. Utsi wonunkhira wa zofukizazo unali kukwera m’mwamba.+
8 Kenako Hilikiya+ mkulu wa ansembe anauza Safani+ mlembi+ kuti: “Ndapeza buku la chilamulo+ m’nyumba ya Yehova!” Choncho Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani, ndipo iye anayamba kuliwerenga.
14 Iwo anatuma anthuwo kuti akatenge Yeremiya m’Bwalo la Alonda+ ndi kumupereka kwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani,+ kuti apite naye kunyumba kwake, kuti Yeremiyayo akakhale pakati pa anthu akwawo.
11 Ndinaonanso akuluakulu 70+ a nyumba ya Isiraeli ataimirira. Yaazaniya mwana wa Safani+ anali ataima pakati pawo. Iwo anaima pamaso pa zojambulazo, aliyense atanyamula chiwaya chofukizira nsembe m’manja mwake. Utsi wonunkhira wa zofukizazo unali kukwera m’mwamba.+