2 Mbiri 26:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma atangokhala wamphamvu, mtima wake unadzikuza+ mpaka kufika pom’pweteketsa.+ Choncho anachita zosakhulupirika kwa Yehova Mulungu wake ndipo anapita m’kachisi wa Yehova kukafukiza paguwa lansembe zofukiza.+ Yeremiya 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi mungamabe,+ kupha,+ kuchita chigololo,+ kulumbira monama,+ kufukiza nsembe zautsi kwa Baala+ ndi kutsatira milungu ina imene simunali kuidziwa,+ Ezekieli 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Unali kutenganso zovala zako za nsalu yopeta n’kuphimbira zifanizirozo. Komanso unkaika mafuta anga ndi zonunkhiritsa zanga+ pamaso pa zifanizirozo.
16 Koma atangokhala wamphamvu, mtima wake unadzikuza+ mpaka kufika pom’pweteketsa.+ Choncho anachita zosakhulupirika kwa Yehova Mulungu wake ndipo anapita m’kachisi wa Yehova kukafukiza paguwa lansembe zofukiza.+
9 Kodi mungamabe,+ kupha,+ kuchita chigololo,+ kulumbira monama,+ kufukiza nsembe zautsi kwa Baala+ ndi kutsatira milungu ina imene simunali kuidziwa,+
18 Unali kutenganso zovala zako za nsalu yopeta n’kuphimbira zifanizirozo. Komanso unkaika mafuta anga ndi zonunkhiritsa zanga+ pamaso pa zifanizirozo.