3 M’chaka cha 18 cha Mfumu Yosiya, mfumuyo inatuma Safani+ mwana wa Azaliya mwana wa Mesulamu yemwe anali mlembi, kuti apite kunyumba ya Yehova. Inam’tuma ndi mawu akuti:
8 M’chaka cha 18+ cha ulamuliro wake, atayeretsa dzikolo ndi nyumba ya Mulungu, iye anatuma Safani+ mwana wa Azaliya, Maaseya mkulu wa mzinda, ndi Yowa mwana wa Yowahazi wolemba zochitika, kuti akakonze+ nyumba ya Yehova Mulungu wake.