Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma Asa anamukwiyira wamasomphenyayo. Kenako anamuika m’ndende n’kumumanga m’matangadza+ popeza anamupsera mtima kwambiri chifukwa cha nkhani imeneyi.+ Pa nthawi yomweyo, Asa anayamba kuponderezanso+ anthu ake ena.

  • Yeremiya 20:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako Pasuri anamenya mneneri Yeremiya+ ndi kumuika m’matangadza+ amene anali pa Chipata Chakumtunda cha Benjamini, cha m’nyumba ya Yehova.

  • Machitidwe 5:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 ndi kugwira atumwiwo n’kuwatsekera m’ndende.+

  • Machitidwe 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano Herode atakonzeka kuti abweretse Petulo kwa anthu, usiku umenewo Petuloyo anali chigonere ali womangidwa ndi maunyolo awiri pakati pa asilikali awiri. Pakhomo panalinso alonda olondera ndende.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena