Yeremiya 38:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inatumiza anthu kuti akatenge mneneri Yeremiya ndi kubwera naye kwa iye+ pakhomo lachitatu+ la m’nyumba ya Yehova.+ Yeremiya atafika, mfumu inamuuza kuti: “Ndikufuna ndikufunse. Usandibisire kalikonse.”+
14 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inatumiza anthu kuti akatenge mneneri Yeremiya ndi kubwera naye kwa iye+ pakhomo lachitatu+ la m’nyumba ya Yehova.+ Yeremiya atafika, mfumu inamuuza kuti: “Ndikufuna ndikufunse. Usandibisire kalikonse.”+