Ezekieli 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Lira ndi kufuula+ iwe mwana wa munthu, chifukwa lupangalo laukira anthu anga.+ Laukira atsogoleri onse a Isiraeli.+ Atsogoleriwo aperekedwa kuti aphedwe ndi lupanga pamodzi ndi anthu anga.+ Chotero menya pantchafu yako chifukwa cha chisoni.+
12 “‘Lira ndi kufuula+ iwe mwana wa munthu, chifukwa lupangalo laukira anthu anga.+ Laukira atsogoleri onse a Isiraeli.+ Atsogoleriwo aperekedwa kuti aphedwe ndi lupanga pamodzi ndi anthu anga.+ Chotero menya pantchafu yako chifukwa cha chisoni.+