Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako gulu lonse lankhondo la Akasidi, lomwe linali ndi mkulu wa asilikali olondera mfumu uja, linagwetsa mpanda wonse wa Yerusalemu.+

  • Nehemiya 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chotero anandiuza kuti: “Anthu otsala amene ali m’chigawo,*+ amene anathawa ku ukapolo, ali pamavuto aakulu+ ndipo akunyozedwa.+ Nawonso mpanda+ wa Yerusalemu unagwa ndipo zipata+ zake zinatenthedwa ndi moto.”

  • Yeremiya 52:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako gulu lonse lankhondo la Akasidi, lomwe linali ndi mkulu wa asilikali olondera mfumu uja, linagwetsa mpanda wonse wa Yerusalemu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena