2 Mafumu 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anasiya malamulo onse+ a Yehova Mulungu wawo n’kudzipangira zifaniziro ziwiri za ana a ng’ombe,+ zopangidwa ndi zitsulo zosungunula,+ komanso mzati wopatulika.+ Anayamba kugwadira khamu lonse la zinthu zakuthambo+ ndi kutumikira Baala.+ Nehemiya 9:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mafumu athu, akalonga athu, ansembe athu ndi makolo athu+ sanatsatire chilamulo chanu+ ndipo sanamvere malamulo anu+ kapena zikumbutso zanu zowachenjeza.+ Salimo 106:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tachimwa mofanana ndi makolo athu.+Tachita zinthu zosayenera, tachita zinthu zoipa.+
16 Anasiya malamulo onse+ a Yehova Mulungu wawo n’kudzipangira zifaniziro ziwiri za ana a ng’ombe,+ zopangidwa ndi zitsulo zosungunula,+ komanso mzati wopatulika.+ Anayamba kugwadira khamu lonse la zinthu zakuthambo+ ndi kutumikira Baala.+
34 Mafumu athu, akalonga athu, ansembe athu ndi makolo athu+ sanatsatire chilamulo chanu+ ndipo sanamvere malamulo anu+ kapena zikumbutso zanu zowachenjeza.+