Miyambo 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova adzagwetsa nyumba za anthu odzikuza,+ koma adzakhazikitsa malire a malo a mkazi wamasiye.+ Amosi 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Akakumba Manda* kuti abisale mmenemo ndidzawatulutsa ndi dzanja langa,+ ndipo akakwera kumwamba ndidzawatsitsira pansi.+ Obadiya 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale malo ako atakhala pamwamba ngati a chiwombankhanga, kapena ngakhale utamanga chisa chako pakati pa nyenyezi, ine ndidzakugwetsa kuchokera pamenepo,”+ watero Yehova.
2 Akakumba Manda* kuti abisale mmenemo ndidzawatulutsa ndi dzanja langa,+ ndipo akakwera kumwamba ndidzawatsitsira pansi.+
4 Ngakhale malo ako atakhala pamwamba ngati a chiwombankhanga, kapena ngakhale utamanga chisa chako pakati pa nyenyezi, ine ndidzakugwetsa kuchokera pamenepo,”+ watero Yehova.