Salimo 139:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngati ndingakwere kumwamba, inu mudzakhala komweko.+Ndipo ngati ndingayale bedi langa ku Manda, taonani! inunso mudzakhala komweko.+ Miyambo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Manda ndiponso malo a chiwonongeko+ zili pamaso pa Yehova.+ Ndiye kuli bwanji mitima ya ana a anthu?+
8 Ngati ndingakwere kumwamba, inu mudzakhala komweko.+Ndipo ngati ndingayale bedi langa ku Manda, taonani! inunso mudzakhala komweko.+
11 Manda ndiponso malo a chiwonongeko+ zili pamaso pa Yehova.+ Ndiye kuli bwanji mitima ya ana a anthu?+