4 Ndiyeno khoma la mzindawo linabooledwa,+ ndipo amuna onse ankhondo anathawa usiku kudzera pachipata chimene chinali pakati pa makoma awiri, pafupi ndi munda wa mfumu.+ Akasidi+ anali atazungulira mzinda wonsewo, ndipo mfumuyo inayamba kuthawa+ kulowera cha ku Araba.+