17 “Ndiyeno uwauze kuti, ‘Maso anga atulutse misozi usiku ndi usana ndipo asasiye kutulutsa misozi,+ pakuti pamveka kugunda kwakukulu ndipo namwali, mwana wamkazi wa anthu anga wawonongedwa.+ Iye wawonongedwa ndi chilonda chachikulu cha mkwapulo chosachiritsika.+