Yoweli 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mitundu ya anthu idzamva ululu waukulu+ chifukwa cha mtunduwo, ndipo nkhope zawo zonse zidzakhala zankhawa.+ Nahumu 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mzindawu auchititsa kukhala wopanda kanthu ndipo ausandutsa bwinja.+ Mitima yawo yasungunuka ndi mantha.+ Mawondo awo akunjenjemera+ ndipo akumva ululu thupi lonse.+ Nkhope zawo zonse zili ndi nkhawa.+
6 Mitundu ya anthu idzamva ululu waukulu+ chifukwa cha mtunduwo, ndipo nkhope zawo zonse zidzakhala zankhawa.+
10 Mzindawu auchititsa kukhala wopanda kanthu ndipo ausandutsa bwinja.+ Mitima yawo yasungunuka ndi mantha.+ Mawondo awo akunjenjemera+ ndipo akumva ululu thupi lonse.+ Nkhope zawo zonse zili ndi nkhawa.+