Yeremiya 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinayang’anitsitsa koma sindinaone munthu aliyense. Ndipo zolengedwa zonse zouluka zinali zitathawa.+ Hoseya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 N’chifukwa chake dzikoli lidzalira maliro+ ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalefukiratu pamodzi ndi zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga. Nsomba zam’nyanja nazonso zidzafa.+ Zefaniya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ndidzafafaniza anthu ndi nyama.+ Ndidzafafaniza zolengedwa zouluka m’mlengalenga, nsomba za m’nyanja,+ zokhumudwitsa pamodzi ndi anthu oipa,+ ndipo ndidzawononga anthu onse ndi kuwachotsa panthaka,”+ watero Yehova.
25 Ndinayang’anitsitsa koma sindinaone munthu aliyense. Ndipo zolengedwa zonse zouluka zinali zitathawa.+
3 N’chifukwa chake dzikoli lidzalira maliro+ ndipo aliyense wokhala mmenemo adzalefukiratu pamodzi ndi zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka m’mlengalenga. Nsomba zam’nyanja nazonso zidzafa.+
3 “Ndidzafafaniza anthu ndi nyama.+ Ndidzafafaniza zolengedwa zouluka m’mlengalenga, nsomba za m’nyanja,+ zokhumudwitsa pamodzi ndi anthu oipa,+ ndipo ndidzawononga anthu onse ndi kuwachotsa panthaka,”+ watero Yehova.