Genesis 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+ Deuteronomo 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Ndiyeno mukapitiriza kumvera zigamulo zimenezi ndi kuzisunga,+ Yehova Mulungu wanu adzasunga pangano+ ndi kukusonyezani kukoma mtima kosatha, zimene analumbirira makolo anu.+ Salimo 105:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wakumbukira pangano limene anapangana ndi Abulahamu,+Ndi lonjezo limene analumbira kwa Isaki,+
18 Pa tsiku limeneli Yehova anachita pangano ndi Abulamu,+ kuti: “Dziko ili ndidzalipereka kwa mbewu yako,+ kuyambira kumtsinje wa ku Iguputo mpaka kumtsinje waukulu, mtsinje wa Firate.+
12 “Ndiyeno mukapitiriza kumvera zigamulo zimenezi ndi kuzisunga,+ Yehova Mulungu wanu adzasunga pangano+ ndi kukusonyezani kukoma mtima kosatha, zimene analumbirira makolo anu.+