Salimo 89:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma inu mwataya wodzozedwa wanu moti mukupitiriza kunyansidwa naye,+Ndipo mwamukwiyira.+ Maliro 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma inu mwatikanitsitsa.+ Mwatikwiyira kwambiri.+