Yesaya 41:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usachite mantha, pakuti ndili nawe.+ Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa.+ Ndithu ndikuthandiza.+ Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja+ lachilungamo.’+ Machitidwe 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 chifukwa ine ndili nawe.+ Palibe munthu amene adzakukhudze ndi kukuvulaza, pakuti ndili ndi anthu ambiri mumzinda uno.”
10 Usachite mantha, pakuti ndili nawe.+ Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa.+ Ndithu ndikuthandiza.+ Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja+ lachilungamo.’+
10 chifukwa ine ndili nawe.+ Palibe munthu amene adzakukhudze ndi kukuvulaza, pakuti ndili ndi anthu ambiri mumzinda uno.”