1 Samueli 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Hana anayankha kuti: “Ayi mbuyanga! Ine ndine mkazi wopsinjika maganizo. Sindinamwe vinyo kapena chakumwa choledzeretsa ayi, koma ndikufotokoza nkhawa zanga zonse kwa Yehova.+ Salimo 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.] Salimo 142:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinapitirizabe kumukhuthulira nkhawa zanga.+Ndinapitirizabe kumuuza masautso anga.+
15 Pamenepo Hana anayankha kuti: “Ayi mbuyanga! Ine ndine mkazi wopsinjika maganizo. Sindinamwe vinyo kapena chakumwa choledzeretsa ayi, koma ndikufotokoza nkhawa zanga zonse kwa Yehova.+
8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.]