1 Samueli 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Musachititse kapolo wanu wamkazi kukhala ngati mkazi wopanda pake,+ popeza ndikulankhulabe mpaka pano chifukwa cha kuchuluka kwa nkhawa ndi nsautso.”+ Yesaya 26:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inu Yehova, pa nthawi ya masautso iwo atembenukira kwa inu.+ Mutawalanga, akhuthulira mitima yawo kwa inu m’pemphero lonong’ona.+ Mateyu 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho atapita patsogolo pang’ono, anagwada mpaka nkhope yake pansi, ndipo anapemphera+ kuti: “Atate wanga, ngati n’kotheka, kapu+ iyi indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga,+ koma mwa kufuna kwanu.”+
16 Musachititse kapolo wanu wamkazi kukhala ngati mkazi wopanda pake,+ popeza ndikulankhulabe mpaka pano chifukwa cha kuchuluka kwa nkhawa ndi nsautso.”+
16 Inu Yehova, pa nthawi ya masautso iwo atembenukira kwa inu.+ Mutawalanga, akhuthulira mitima yawo kwa inu m’pemphero lonong’ona.+
39 Choncho atapita patsogolo pang’ono, anagwada mpaka nkhope yake pansi, ndipo anapemphera+ kuti: “Atate wanga, ngati n’kotheka, kapu+ iyi indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga,+ koma mwa kufuna kwanu.”+