Oweruza 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Aisiraeli,+ moti anawagulitsa+ kwa Kusani-risataimu, mfumu ya Mesopotamiya.+ Ana a Isiraeli anatumikira Kusani-risataimu zaka 8. Aheberi 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo mwaiwaliratu langizo lokudandaulirani limene limakutchani ana,+ lakuti: “Mwana wanga, usapeputse chilango* cha Yehova, kapena kutaya mtima pamene iye akukudzudzula.+ Aheberi 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+
8 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Aisiraeli,+ moti anawagulitsa+ kwa Kusani-risataimu, mfumu ya Mesopotamiya.+ Ana a Isiraeli anatumikira Kusani-risataimu zaka 8.
5 Ndipo mwaiwaliratu langizo lokudandaulirani limene limakutchani ana,+ lakuti: “Mwana wanga, usapeputse chilango* cha Yehova, kapena kutaya mtima pamene iye akukudzudzula.+
6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+