Levitiko 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine ndidzakukanani,* ndipo adani anu adzakugonjetsani+ ndi kukuponderezani,+ moti muzidzathawa popanda munthu wokuthamangitsani.+ Oweruza 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+ 1 Samueli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atatero iwo anaiwala Yehova Mulungu wawo,+ moti anawagulitsa+ kwa Sisera+ mkulu wa gulu lankhondo la Hazori, komanso kwa Afilisiti+ ndi kwa mfumu ya Mowabu,+ ndipo onsewa anapitiriza kumenyana nawo.
17 Ine ndidzakukanani,* ndipo adani anu adzakugonjetsani+ ndi kukuponderezani,+ moti muzidzathawa popanda munthu wokuthamangitsani.+
14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+
9 Atatero iwo anaiwala Yehova Mulungu wawo,+ moti anawagulitsa+ kwa Sisera+ mkulu wa gulu lankhondo la Hazori, komanso kwa Afilisiti+ ndi kwa mfumu ya Mowabu,+ ndipo onsewa anapitiriza kumenyana nawo.