Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamenepo ana a Isiraeli anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize.+ Iwo anati: “Takuchimwirani+ inu Mulungu wathu, chifukwa takusiyani ndipo tikutumikira Abaala.”+

  • Salimo 77:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Pa tsiku la zowawa zanga ndafunafuna Yehova.+

      Ndakweza dzanja langa kumwamba usiku wonse, ndipo silinachite dzanzi.

      Koma sindinatonthozeke.+

  • Salimo 78:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Nthawi zonse akayamba kuwapha, iwo anali kumufunafuna.+

      Anali kutembenuka ndi kuyamba kufunafuna Mulungu.+

  • Hoseya 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako ndidzabwerera kumalo anga kufikira iwo atalangidwa chifukwa cha zolakwa zawo+ ndipo adzayamba kufunafuna nkhope yanga.+ Zinthu zikadzawavuta,+ adzandifuna.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena