Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 42:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ndidzakumbukira zinthu zakale ndipo moyo wanga udzavutika pokumbukira zimenezo.+

      Pakuti ndinali kuyenda ndi khwimbi la anthu,

      Ndinali kuyenda pang’onopang’ono patsogolo pawo kupita kunyumba ya Mulungu,+

      Tinali kufuula mosangalala ndi kuyamika Mulungu.+

      Khamu la anthu okondwerera madyerero linali kunditsatira.+

  • Salimo 42:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Inu Mulungu wanga, ine ndataya mtima.+

      N’chifukwa chake ndakumbukira inu,+

      Pamene ndili m’dziko la Yorodano ndi m’mapiri a Herimoni,+

      Pamene ndili m’phiri laling’ono.+

  • Salimo 62:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+

      Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+

      Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.]

  • Salimo 142:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ndinapitirizabe kumukhuthulira nkhawa zanga.+

      Ndinapitirizabe kumuuza masautso anga.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena