Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 16:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndipo uzisangalala pa chikondwerero chimenecho,+ iweyo, mwana wako wamwamuna, mwana wako wamkazi, kapolo wako wamwamuna, kapolo wako wamkazi, Mlevi, mlendo wokhala pakati panu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye, amene ali mumzinda wanu.

  • Aefeso 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mukakhala pakati panu muziimba masalimo,+ nyimbo zotamanda+ Mulungu, ndiponso nyimbo zauzimu. Muziimba+ nyimbo zotamanda+ Yehova m’mitima mwanu,

  • Akolose 3:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mawu a Khristu akhazikike mwa inu ndipo akupatseni nzeru zonse.+ Pitirizani kuphunzitsana+ ndi kulangizana mwa masalimo,+ nyimbo zotamanda Mulungu, ndi nyimbo zauzimu+ zogwira mtima. Pitirizani kuimbira Yehova+ m’mitima yanu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena