Yesaya 51:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ana ako akomoka.+ Agona m’misewu yonse ngati nkhosa zakutchire zokodwa mu ukonde,+ ngati anthu okhuta mkwiyo wa Yehova,+ okhuta kudzudzula kwa Mulungu wako.”+ Maliro 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amene anaphedwa ndi lupanga+ aliko bwino kusiyana ndi amene anafa ndi njala,+Pakuti amene anafa ndi njala anafooka chifukwa chosowa chakudya, ndipo anakhala ngati apyozedwa ndi lupanga. Ezekieli 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ndikadzakutumizirani mivi yakupha yobweretsa njala+ imene idzakuwonongeni,+ ndidzachititsa kuti njala ikule pakati panu, ndipo ndidzathyola ndodo zimene mumakolowekapo mikate yozungulira yoboola pakati.+
20 Ana ako akomoka.+ Agona m’misewu yonse ngati nkhosa zakutchire zokodwa mu ukonde,+ ngati anthu okhuta mkwiyo wa Yehova,+ okhuta kudzudzula kwa Mulungu wako.”+
9 Amene anaphedwa ndi lupanga+ aliko bwino kusiyana ndi amene anafa ndi njala,+Pakuti amene anafa ndi njala anafooka chifukwa chosowa chakudya, ndipo anakhala ngati apyozedwa ndi lupanga.
16 “‘Ndikadzakutumizirani mivi yakupha yobweretsa njala+ imene idzakuwonongeni,+ ndidzachititsa kuti njala ikule pakati panu, ndipo ndidzathyola ndodo zimene mumakolowekapo mikate yozungulira yoboola pakati.+