Salimo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzafuulira Yehova mokweza,Ndipo iye adzandiyankha m’phiri lake loyera.+ [Seʹlah.] Salimo 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndichokereni pamaso panga inu nonse ochita zopweteka ena,+Chifukwa Yehova adzamva ndithu mawu a kulira kwanga.+ Salimo 116:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 116 Mtima wanga ndi wodzaza ndi chikondi, chifukwa Yehova amamva+Mawu anga ndi madandaulo anga.+
8 Ndichokereni pamaso panga inu nonse ochita zopweteka ena,+Chifukwa Yehova adzamva ndithu mawu a kulira kwanga.+