Genesis 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iye anawononga mizindayi, ngakhale Chigawo chonsecho ndi anthu onse a m’mizindayi, kuphatikizapo zomera za panthaka.+ Danieli 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu munachitadi zimene munachenjeza kuti mudzatichitira,+ ifeyo ndi atsogoleri athu.+ Munatigwetsera tsoka lalikulu ndipo tsoka limene lagwera Yerusalemu silinachitikeponso padziko lonse lapansi.+
25 Iye anawononga mizindayi, ngakhale Chigawo chonsecho ndi anthu onse a m’mizindayi, kuphatikizapo zomera za panthaka.+
12 Inu munachitadi zimene munachenjeza kuti mudzatichitira,+ ifeyo ndi atsogoleri athu.+ Munatigwetsera tsoka lalikulu ndipo tsoka limene lagwera Yerusalemu silinachitikeponso padziko lonse lapansi.+