Zekariya 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Sindidzachitiranso chifundo anthu okhala m’dzikoli,’+ watero Yehova. ‘Choncho ine ndichititsa aliyense kuti aponderezedwe ndi mnzake+ ndiponso mfumu yake.+ Iwo adzawononga dzikoli, ndipo ine sindidzapulumutsa aliyense m’manja mwawo.’”+
6 “‘Sindidzachitiranso chifundo anthu okhala m’dzikoli,’+ watero Yehova. ‘Choncho ine ndichititsa aliyense kuti aponderezedwe ndi mnzake+ ndiponso mfumu yake.+ Iwo adzawononga dzikoli, ndipo ine sindidzapulumutsa aliyense m’manja mwawo.’”+