Salimo 102:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma inu simudzasintha, ndipo mudzakhalapo kwamuyaya.+ Salimo 145:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ufumu wanu ndi ufumu umene udzakhalapobe mpaka kalekale.+Ulamuliro wanu udzakhalapobe ku mibadwo yonse.+ Salimo 146:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova adzakhala mfumu mpaka kalekale,+Mulungu wako, iwe Ziyoni, adzakhala mfumu ku mibadwomibadwo.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Habakuku 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Yehova, inutu mwakhalapo kuyambira kalekale.+ Inu Mulungu wanga, Mulungu wanga Woyera, inu simufa.+ Inu Yehova, mwaika Akasidi pamalo oti muwaweruze. Inu Thanthwe,+ mwasankha kuti mutidzudzule.+
13 Ufumu wanu ndi ufumu umene udzakhalapobe mpaka kalekale.+Ulamuliro wanu udzakhalapobe ku mibadwo yonse.+
10 Yehova adzakhala mfumu mpaka kalekale,+Mulungu wako, iwe Ziyoni, adzakhala mfumu ku mibadwomibadwo.+Tamandani Ya, anthu inu!+
12 Inu Yehova, inutu mwakhalapo kuyambira kalekale.+ Inu Mulungu wanga, Mulungu wanga Woyera, inu simufa.+ Inu Yehova, mwaika Akasidi pamalo oti muwaweruze. Inu Thanthwe,+ mwasankha kuti mutidzudzule.+