Salimo 147:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yamika Yehova,+ iwe Yerusalemu.Tamanda Mulungu wako, iwe Ziyoni.+ Yoweli 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu,+ amene ndimakhala mu Ziyoni, phiri langa lopatulika.+ Yerusalemu adzakhala malo anga opatulika,+ ndipo alendo sadzadutsanso mmenemo.+
17 Pamenepo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu,+ amene ndimakhala mu Ziyoni, phiri langa lopatulika.+ Yerusalemu adzakhala malo anga opatulika,+ ndipo alendo sadzadutsanso mmenemo.+