Machitidwe 2:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndipo ndi mawu enanso ambiri, Petulo anachitira umboni mokwanira. Komanso sanaleke kuwadandaulira kuti: “Dzipulumutseni ku m’badwo wopotoka maganizo uno.”+ 1 Timoteyo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nthawi zonse uzisamala ndi zimene umachita+ komanso zimene umaphunzitsa.+ Pitiriza kuchita zimenezi, chifukwa ukatero udzadzipulumutsa wekha komanso anthu okumvera.+
40 Ndipo ndi mawu enanso ambiri, Petulo anachitira umboni mokwanira. Komanso sanaleke kuwadandaulira kuti: “Dzipulumutseni ku m’badwo wopotoka maganizo uno.”+
16 Nthawi zonse uzisamala ndi zimene umachita+ komanso zimene umaphunzitsa.+ Pitiriza kuchita zimenezi, chifukwa ukatero udzadzipulumutsa wekha komanso anthu okumvera.+