1 Mafumu 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye adzasiya Isiraeli+ chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita, ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli.”+ 1 Mafumu 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ahabu anachita zinthu zonyansa kwambiri mwa kutsatira mafano onyansa+ monga momwe Aamori, amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli, anachitira.’”+ 2 Mafumu 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zimenezi zinachitika chifukwa chakuti ana a Isiraeli anachimwira+ Yehova Mulungu wawo, yemwe anawatulutsa m’dziko la Iguputo+ n’kuwachotsa m’manja mwa Farao mfumu ya Iguputo, ndipo anayamba kuopa milungu ina.+
16 Iye adzasiya Isiraeli+ chifukwa cha machimo amene Yerobowamu anachita, ndiponso amene anachimwitsa nawo Isiraeli.”+
26 Ahabu anachita zinthu zonyansa kwambiri mwa kutsatira mafano onyansa+ monga momwe Aamori, amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli, anachitira.’”+
7 Zimenezi zinachitika chifukwa chakuti ana a Isiraeli anachimwira+ Yehova Mulungu wawo, yemwe anawatulutsa m’dziko la Iguputo+ n’kuwachotsa m’manja mwa Farao mfumu ya Iguputo, ndipo anayamba kuopa milungu ina.+