Salimo 119:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Chititsani maso anga kuti asaone zinthu zopanda pake.+Ndiyendetseni m’njira yanu kuti ndikhalebe wamoyo.+ Mateyu 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+ 1 Yohane 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti chilichonse cha m’dziko,+ monga chilakolako cha thupi,+ chilakolako cha maso+ ndi kudzionetsera ndi zimene munthu ali nazo pa moyo wake,+ sizichokera kwa Atate, koma kudziko.+
37 Chititsani maso anga kuti asaone zinthu zopanda pake.+Ndiyendetseni m’njira yanu kuti ndikhalebe wamoyo.+
28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+
16 Pakuti chilichonse cha m’dziko,+ monga chilakolako cha thupi,+ chilakolako cha maso+ ndi kudzionetsera ndi zimene munthu ali nazo pa moyo wake,+ sizichokera kwa Atate, koma kudziko.+