-
Hoseya 1:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 M’masiku amenewo, Yehova anayamba kulankhula kudzera mwa Hoseya, ndipo Yehova anauza Hoseya kuti: “Pita+ ukakwatire mkazi amene adzachita dama. Pamenepo udzakhala ndi ana chifukwa cha dama la mkazi wakoyo. Pakuti mwanjira yofanana ndi zimenezi, dzikoli latembenuka ndi kusiya kutsatira Yehova chifukwa cha dama.”+
-