Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Ine ndidzakumanga ndi zingwe+ kuti usatembenukire kumbali ina, mpaka utamaliza masiku ako ozungulira mzindawo.

  • Yohane 21:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndithudi ndikukuuza iwe, Pamene unali mnyamata, unali kuvala wekha ndi kupita kumene unali kufuna. Koma ukadzakalamba, udzatambasula manja ako ndipo munthu wina adzakuveka,+ ndi kukunyamula kupita nawe kumene iwe sukufuna.”+

  • Machitidwe 20:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Chimodzi chokha chimene ndikudziwa n’chakuti mumzinda ndi mzinda, mzimu woyera+ wandichitira umboni mobwerezabwereza kuti maunyolo ndi masautso akundiyembekezera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena