Ezekieli 30:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumuyo ndi anthu ake, olamulira ankhanza a mitundu ina ya anthu,+ akubwera kudzawononga dzikolo kuti likhale bwinja. Iwo adzasolola malupanga awo kumenyana ndi Iguputo ndipo adzadzaza dzikolo ndi anthu ophedwa.+
11 Mfumuyo ndi anthu ake, olamulira ankhanza a mitundu ina ya anthu,+ akubwera kudzawononga dzikolo kuti likhale bwinja. Iwo adzasolola malupanga awo kumenyana ndi Iguputo ndipo adzadzaza dzikolo ndi anthu ophedwa.+