Yesaya 34:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu awo ophedwa adzatayidwa, ndipo fungo loipa la mitembo yawo lidzakwera m’mwamba.+ Mapiri adzasungunuka chifukwa cha magazi awo.+ Ezekieli 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwe ndidzakutaya m’chipululu pamodzi ndi nsomba zonse za m’ngalande za Nailo.+ Udzagwera panthaka+ ndipo palibe amene adzakutenge kukakuika m’manda. Ndidzakupereka kwa zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka kuti ukhale chakudya chawo.+
3 Anthu awo ophedwa adzatayidwa, ndipo fungo loipa la mitembo yawo lidzakwera m’mwamba.+ Mapiri adzasungunuka chifukwa cha magazi awo.+
5 Iwe ndidzakutaya m’chipululu pamodzi ndi nsomba zonse za m’ngalande za Nailo.+ Udzagwera panthaka+ ndipo palibe amene adzakutenge kukakuika m’manda. Ndidzakupereka kwa zilombo zakutchire ndi zolengedwa zouluka kuti ukhale chakudya chawo.+